Mavesi a m'Baibulo Onena za Gwiritsitsani

Mavesi 5 a m'Baibulo onena za Gwiritsitsani oti muwerenge, musinkhasinkhe, ndi kuloweza.

01 Ahebri 10:23

Tiyeni tigwiritsitse mosagwedezeka zimene timaziyembekezera ndi kuzivomereza, pakuti amene anatilonjezayo ndi wokhulupirika.

02 Ahebri 3:14

Pakuti timakhala anzake a Khristu, ngati tigwiritsitsa mpaka potsiriza chitsimikizo chimene tinali nacho pachiyambi.

03 1 Atesalonika 5:21

Yesani zinthu zonse. Gwiritsitsani chimene ndi chabwino.

04 Chivumbulutso 3:11

Ine ndikubwera msanga. Gwiritsitsa chimene uli nacho kuti wina angakulande chipewa chako chaufumu.

05 Afilipi 2:16

powawuza mawu amoyo. Ndipo ine ndidzatha kunyadira pa tsiku la Khristu kuti sindinathamange kapena kugwira ntchito pachabe.

Mitu yofanana